NKHANI
Promise Kamwendo yemwe amayenera kusaina mgwirizano wake ndi timu ya FCB Nyasa Big Bullets mtsiku la lero sakuoneka.
Katswiriyu amapita ku Blantyre komwe akanaonetsedwa ndi timu ya FCB Nyasa Big Bullets koma zamveka kuti mafoni ake azimitsidwa.
Zamveka kuti osewerayu watengedwa ku Wanderers kuti akasaine mgwirizano kutimuyi koma ngakhale kuti timu ya Bullets inapereka kale ndalama zake ku Premier Bet Dedza Dynamos zokwana K3 million.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores