Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
KAMWENDO ACHOKA KU DEDZA MWA ULERE
Osewera kutsogolo watimu ya Premier Bet Dedza Dynamos, Promise Kamwendo, wakana mgwirizano watsopano kutimuyi zomwe zikuonetsa kuti achoka mwa ulere kutimu yakeyi.
Wamkulu kutimuyi, Frella Kulemero, watsimikiza za nkhaniyi pomwe wati anakambirana ndi Kamwendo kuti awonjezere mgwirizano wake womwe ukutha pa 31 December 2024 ndipo anavomera koma tsopano wangosintha poyerayera ndipo wati waphunzira phunziro lalikulu pa nkhani.
"Tachilapa, ofunika osewera mwina azionjezera migwirizano yawo kutatsala zaka ziwiri kuti mwina asamatithawe mwaulere mmalo moti tiwapindulire." Anatero Kulemero.
Timuyi inapezeka ikulipira ndalama za nkhaninkhani komanso osapindulako kalikonse pomwe osewerayu ankafunidwa ndi matimu a FCB Nyasa Big Bullets komanso Mighty Mukuru Wanderers zomwe zinakanika patapezeka zolakwika zingapo ndekuti timuyi ifa kawiri.
Chibwererereni ku Dedza kuchokera ku Wanderers, Kamwendo wasewera masewero asanu ndi amodzi ndipo mmasewero omwe apitaw
KAMWENDO STRUGGLES ON DYNAMOS RETURN
Premier Bet Dedza Dynamos hitman, Promise Kamwendo has now gone five straight games without getting a goal since his return to the team after a failed move to Blantyre giants, Mighty Mukuru Wanderers and FCB Nyasa Big Bullets in the mid-season transfer window.
The player has been featured in all five matches since making a return to the team and four of these matches have been starts while one was from the bench.
Coach Andrew Bunya trusted Kamwendo against Creck Sporting Club when he was introduced on 56th minute but it ended 0-0 before being a starter against Silver Strikers in the first leg of the Airtel Top 8 at the Silver Stadium where they lost 4-1.
He was also a starter in 0-1 defeat against Civil Service, in a 2-0 defeat in hands of Kamuzu Barracks and the return leg of the Airtel Top 8 match against Silver Strikers where they lost 2-1.
Before making his controversial issues in the country, Kamwendo scored 11 goals in all competitions.
WANDERERS, DYNAMOS SLAPPED AS KAMWENDO RETURNS TO DEDZA
Football Association of Malawi player status has slapped Premier Bet Dedza Dynamos and Mighty Mukuru Wanderers with heavy fines following a misconduct of the transfer for Promise Kamwendo in the just ended transfer window.
This comes after FCB Nyasa Big Bullets appealed to FAM following a failed deal that saw Kamwendo penning a deal with the Nomads despite already paid a transfer fee to Dedza Dynamos.
In a verdict released today, FAM had ordered the player to return to Dedza as he has a valid contract with the team and that he should return the K6 million which Wanderers gave him as a signing on fee in a space of 14 days.
The Association has further told Dynamos to return back K3 million to FCB Nyasa Big Bullets and K4 million to Mighty Mukuru Wanderers plus a punishment of K3 million for failing to initiate the deal.
Meanwhile, the Nomads will have to pay K4 million for their conduct and that sound be paid in 14 days period
JUST IN
Mighty Mukuru Wanderers has signed Premier Bet Dedza Dynamos forward, Promise Kamwendo.
The team's Chief Executive Officer, Panganeni Ndovi, has just confirmed about the deal.
The player has signed a three year contract with the Lali Lubani side after making a U-turn to join FCB Nyasa Big Bullets as earlier planned.
NKHANI
Promise Kamwendo yemwe amayenera kusaina mgwirizano wake ndi timu ya FCB Nyasa Big Bullets mtsiku la lero sakuoneka.
Katswiriyu amapita ku Blantyre komwe akanaonetsedwa ndi timu ya FCB Nyasa Big Bullets koma zamveka kuti mafoni ake azimitsidwa.
Zamveka kuti osewerayu watengedwa ku Wanderers kuti akasaine mgwirizano kutimuyi koma ngakhale kuti timu ya Bullets inapereka kale ndalama zake ku Premier Bet Dedza Dynamos zokwana K3 million.
NEWS
FCB Nyasa Big Bullets has reached an agreement with Premier Bet Dedza Dynamos to sign their deadly forward, Promise Kamwendo.
It is understood that the deal with be finalized next week as per Wa Mpira reports.
Meanwhile, the People's team have already paid part of the money for the transfer fee of the towering forward.