NEWS
Khuda Muyaba atha kupita mdziko la Jordan kutimu ya Al Jazeera FC mwezi wa mawa pomwe wamvana zonse ndi timuyi.
Izi zikudza atachoka kutimu ya Richards Bay FC yaku South Africa komwe wasewerako miyezi isanu yokha basi.
Source: Mikozi
Kuchepa kwandalama kutifooketsadi mwina dandauloli litaveka padzikhala mpikisano paground.
Takumvani, koma tikubweretsa mipiksano ina kuti muzikhala ndi mwayi wopikisana nawo munjira zosiyana-siyana.
Admin yankhani zomwe anthu akupempha kuti zanveka zitheka kapena ayi. Ndiye ngati zitheke tidikile kuwonjezela mpaka liti? Osati zamipiksano inazoyi izozo tidzawona mukayambitsa.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores