Timu ya Blue Eagles lero isewera ndi Karonga Select ngati njira imodzi yofalitsa uthenga polimbana ndi mchitidwe wa anthu ena kutengera malamulo manja mwawo.
Masewero-wa achitikira pa bwalo la Karonga.
Mphunzitsi wa timu ya Blue Eagles wati agwilitsa ntchito mpata-wu popeza osewera atsopano a timuyi.
Zilibho
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores