Timu ya Silver Strikers yati sipangaso apilo chigamulo cha FAM molingana ndi nkhani ya wosewera yemwe amafuna, Babatunde Adepoju.

Daniel Dauda wa Silver Strikers watsimikiza za nkhaniyi.

19 May 07:37

Share on Facebook
Post Predictions & Updates

Login with Facebook to post predictions, updates & live scores