Timu ya Wanderers yasankha Foster Namwera kukhala oyang'anira osewera a timuyi, Team Manager m'chingerezi.

Mlembi wa komiti yaikulu ya Wanderers, Victor Maunde, watsimikiza za nkhaniyi.

13 Feb 06:51

Share on Facebook
Post Predictions & Updates

Login with Facebook to post predictions, updates & live scores