Chisankho cha Wanderers chatha ndi chisokonezo pomwe panali kusamvana pa anthu omwe apambana pa chisankho-chi.
Owinna yapeza kuti panali mapanza omwe amamenya anthu ena pa chisankho-chi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores