Pamene patsala maola chabe kuti chisankho cha komiti yoyendetsa Wanderers chichitike zadziwika kuti anthu akapikisana pa udindo umodzi okha pomwe maudindo ena anthu alibe oti akapikisana naye.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores