Mlembi wa masapota wa BE FORWARD Wanderers, Samuel Mponda, wapempha akuluakulu a timuyi kuti afulumize kuchititsa chisankho chosankha adindo atsopano oyendetsa timuyi.
A Mponda ati izi zithandizira kuti timuyi iyambe zokonzekera zake nthawi ya bwino.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores