Anthu ochita malonda ku Lilongwe ayamba kukumba pa bwalo la Lilongwe Community kuika malo awo ogulitsira malonda.
Izi zikuchitika kutsatira kuuzidwa ndi khonsolo ya mzinda-wu.
FIFA is encouraging people to follow precaution measures set by the World Health Organisation (WHO) against Covid-19.
The governing football association says people should as well do exercise.
Otsatira matimu a BE FORWARD Wanderers, Nyasa Big Bullets komanso Silver Strikers ati zikhala zowavuta kuthandiza matimu-wa kutengera kuti nawo akhudzidwa ndi mliri wa Covid-19.
Osewera wakale wa Nyasa Big Bullets, Fischer Kondowe, wati akulingalirabe zoti achite kutsatira kuuzidwa ndi akuluakulu a timuyi kuti asiye mpira.
BE FORWARD Wanderers players on Friday continued with individual indoor training.
Reports indicate that the players are told what to do during each particular training session.
Timu ya BE FORWARD Wanderers yati ikhazikitsa njira zapadera zoti masapota a timuyi agwiritse ntchito popereka thandizo la ndalama ku timuyi.
Mfumu ya mzinda wa Lilongwe, Juliana Kaduya, yapereka bwalo la Lilongwe Community kwa ochita malonda kuti azigwilitsa ntchito pamene dziko lino lakhudzidwa ndi Covid-19.
TNM Super League and Flames players have complied to commence individual trainings amid the Corona Virus.
One of the players practicing at his home is Rafiq Namwera of Wanderers.
Flames has maintained its position on the latest FIFA rankings.
Flames is on position 123.
Supporters of BE FORWARD Wanderers residing in Japan have urged football fans in Malawi and the public to listen and follow instructions set by the Ministry of Health.