Timu ya Ekhaya yatsimikiza kuti mphunzitsi wawo Enos Chatama wachoka pa ntchito yake kutimuyi.
Izi zikuchitika pomwe timuyi yatenga chikho cha Airtel Top 8 komabe yakhala ikuvutika mu ligi pomwe yatha pafupifupi miyezi iwiri opanda chipambano.
Chatama anayimitsidwapo ndi timuyi mmbuyomu kutsatira kuyamba mwa udyo kwa timuyi mu ligi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores