Katswiri yemwe amasewera mdziko la England, Shaquille Gwengwe, wachoka kutimu ya Poole Town komwe anangokhalako Kwa chaka chimodzi.
Katswiriyu anali wodalilika kutimuyi kamba koti anakwanitsa kugoletsa zigoli 45 mu masewero omwe wasewera mu zikho zonse ndi timuyi.
Aphunzitsi a timuyi ati kunalidi kovuta kuti akwanitse kusunga katswiriyu kamba ka momwe anasewerera ndipo ati amusowa kwambiri.
Pakadali pano, timu imene osewerayu akupita sikudziwika koma ikhala yamu ligi yapamwapako kusiyana ndi momwe amasewera.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores