Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
WANDERERS NDI CHITIPA KACHIKENANSO
Matimu a Mighty Mukuru Wanderers ndi Chitipa United ndi omwe ayikidwa kuti adzakumane pa mwambo okumbukira tsiku lomwe dziko lino linatenga ufulu ozilamulira tokha, pa 06 July, ku bwalo la Bingu.
Mmodzi mwa atolankhani athu, auzidwa ndi osewera wina wa Chitipa yemwe anati asatchulidwe dzina koma anati ndi chilimbikitso kwa iwo monga timu yaying'ono kukasewera masewero ngati amenewa.
Matimuwa anakumanapo mu TNM Supa ligi pa bwalo la Kamuzu ndipo Chitipa inapambana 1-0 ndi chigoli cha Miracle Gabeya chodzimwetsa yekha.
Timu ya Mighty Wakawaka Tigers yatenga timu ya Chikwawa Sisters yomwe imasewera mpira wamiyendo koma ali amayi ngati mbali imodzi yokwaniritsa zomwe timu ikuyenera kukhala nazo ngati ikufuna kusewera mu TNM Supa ligi.
Mkulu wa timuyi, Robin Alufandika anatsimikiza za nkhaniyi ndipo wati timuyi izichedwa Wakawaka Women's Football Club tsopano.
Timuyi ili ndi matimu a Tigers Reserve komanso Tigers Youth yomwe Ina imasewera mu Under 19 ndipo Ina mu Under 16.
VUNGA'S BRACE SEALS SILVER WIN
Silver Strikers gave up a two goal lead buy restored the lead a minute later as Uchizi Vunga's double fired the Bankers to a 3-2 win over FCB Nyasa Big Bullets during the launch of the Castel Cup at the Bingu National Stadium on Saturday afternoon.
Bullets were down by two goals after 60 minutes but battled it to level the scores on 81st minute but Vunga restored the Bankers lead a minute later to seal the victory for the Bankers.
Bullets started well in the game and Antony Mfune's goal was cancelled out for an offside on 10th minute and the Bankers dominated the game and got a goal through Tathedwa Willard on 45th minute with a long ranger.
The Bankers doubled the scores through Vunga on 55th minute but Bullets made changes that brought fire and Precious Phiri scored on 71st minute with Kajoke levelling 10 minutes later but Vunga restored the lead to seal the win a minute later.
This is the third meeting this year and both have one wins plus a draw.
Gemu ilibwanj
SILVER YAKANA ZOFUNA KUTENGERATU IDANA
Timu ya Silver Strikers yatsutsa mphekesera zomwe zikumveka kuti akukambirana ndi timu yaku Tanzania ya Mbeya City kuti atengeretu katswiri Chimwemwe Idana kuti akhalebe kutimuyi.
Mmodzi mwa akuluakulu atimuyi, Peter Masiye wati zimenezo ndi mphekesera chabe ndipo sakudziwako za nkhaniyi.
Idana akusewera ku Silver Strikers pangongole ndipo wakhala mtima watimuyi pomwe wagoletsa zigoli zinayi ndi kuthandiza zigoli zisanu ndi chimodzi.
Xavier wa Tigers wawina K10,000πΈ atalosera molondolaπ― magemu 11 pa Owinna β½ Monday - Sunday π
Nanunso mungathe kuwina. Loserani magemu ambiri molondola kuposa ena onse pa Owinna.com kuti nanunso muwine sabata iliyonse.
@xavier.kabango titumizireni nambala yanu ya Airtel Money kapena TNM Mpamba kuti mulandire mphoto yanu.
Pepani siinapitedi koma lero yatheka. Tatumiza K10,000 π
Former FCB Nyasa Big Bullets forward, Babatunde Adepoju has declined reports linking him to a transfer to Rwandan elite league side, APR FC.
There were reports from Rwandan journalists saying the star has agreed personal terms with the team and was waiting for his club, Venda Football Academy to agree on a fee.
But commenting on the issue, the incumbent TNM Super League golden boot winner says the reports are not true. The Nigerian left the Malawian champions 6 months ago.
Katswiri wa timu ya Flames, Gabadinho Mhango tsopano ndi oyimilira kampani ya Premier Bet ku nkhani za malonda (brand ambassador) pomwe wasaina mgwirizano wa chaka chimodzi ndi kampaniyi.
TSACHE KU UNA LA NYERERE
Mphekesera yamveka kuti timu ya Mighty Mukuru Wanderers ikufuna kuchotsa Foster Namwera yemwe ndi team manager ndipo akufuna aikepo Yasin Osman.
Timuyinso ikufuna kusesa inu, Alfred Manyozo Jr ndi Chiukepo Msowoya ndi omwe atha kukhudzidwanso pa tsache ili.
Fixture tomorrow
Maghty mukuru wanderers anamuna achayinache t n m super league
Mighty Mukuru Wanderers ikufuna kubweretsanso Joseph Balakasi kutimuyi ndipo akufuna osewera wa Karonga United, Josiah Duwa komanso wina waku Nigeria.
Izi zadza pomwe akuvutika kupambana masewero awo
Mu chaka chino, timuyi yapambana masewero asanu ndipo yagonja kawiri ndikufanana mphamvunso kawiri ndipo ali ndi mapointsi 17 pa nambala yachitatu
Lionel Messi confirms that he will not take part in the 2026 World Cup.
βAs I said earlier, I don't think I will participate in the next World Cup. I haven't changed my mind about that.