Timu ya Mighty Wakawaka Tigers yatenga timu ya Chikwawa Sisters yomwe imasewera mpira wamiyendo koma ali amayi ngati mbali imodzi yokwaniritsa zomwe timu ikuyenera kukhala nazo ngati ikufuna kusewera mu TNM Supa ligi.
Mkulu wa timuyi, Robin Alufandika anatsimikiza za nkhaniyi ndipo wati timuyi izichedwa Wakawaka Women's Football Club tsopano.
Timuyi ili ndi matimu a Tigers Reserve komanso Tigers Youth yomwe Ina imasewera mu Under 19 ndipo Ina mu Under 16.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores