TSACHE KU UNA LA NYERERE
Mphekesera yamveka kuti timu ya Mighty Mukuru Wanderers ikufuna kuchotsa Foster Namwera yemwe ndi team manager ndipo akufuna aikepo Yasin Osman.
Timuyinso ikufuna kusesa inu, Alfred Manyozo Jr ndi Chiukepo Msowoya ndi omwe atha kukhudzidwanso pa tsache ili.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores