Mighty Mukuru Wanderers ikufuna kubweretsanso Joseph Balakasi kutimuyi ndipo akufuna osewera wa Karonga United, Josiah Duwa komanso wina waku Nigeria.
Izi zadza pomwe akuvutika kupambana masewero awo
Mu chaka chino, timuyi yapambana masewero asanu ndipo yagonja kawiri ndikufanana mphamvunso kawiri ndipo ali ndi mapointsi 17 pa nambala yachitatu
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores