Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Fixture ndiye yatuluka mpongo ndani pa malawi chaka chino?
Timothy Chitedze ndi Blessings Kameza tsopano ndi osewera a timu ya Civil Sporting.
Izi zikutsatira ndandanda wa maina omaliza omwe aphunzitsi a timuyi atulutsa.
Timu ya chisodzera ya dziko lino, Malawi U23 yati yakonza kusewera masewero awo ndi Zambia mu mpikisano wa Afcon qualifiers.
Malinga ndi mphunzitsi wa timuyi, Meke Mwase pano zonse zili malo mwake.
Nyasa Big Bullets ikonza mwambo ku mathero kwa mwezi uno ofuna kuthokoza komanso kulimbikitsa osewera omwe anachita bwino season yatha.
Mwambo-wu ukutchedwa Gala Awards m'chingerezi.
Mwambo ukuchedwa Gala Awards m'chingerezi.
Timu ya Silver Strikers yati itulutsa ndandanda wa osewera omwe atumikire timuyi season ya 2019 sabata ya mawa.
Mlembi wa timuyi Lawrence Yobe watsimikiza za nkhaniyi.
Osewera wakale wa timu ya BE FORWARD Wanderers, Khumbo Ng'ambi tsopano ndi osewera wa Moyale Barracks.
Ng'ambi wapita ku timu ya Moyale season yatha atalephera kusewera masewero ochuluka ku Manoma.
Nyasa Big Bullets has released Kondwani Scores Kumwenda as a free agent.
I really like the team of Nyasa bullets.BB it's my best team 4ever
Friendly game ya Silver Strikers vs Songo fc yaku Mozambique ilipo this Saturday?
TNM SUPERLEAGUE FIXTURE 2019
Yapangidwa post check pa ma fixtures
Ernest Tambe tsopano ndi osewera wa timu ya Silver Strikers.
Tambe wasaina contract ya zaka zitatu ndi mabankers-wa.
Timu ya Civil Sporting yachotsa osewera ena ku timuyi atatha sabata ziwiri akuyetsa mwayi.
Dzulo linali tsiku lomaliza lomwe aphunzitsi a timuyi amaona osewera mene akusewelera.
Osewera omwe apita Ku Bullets yaikulu kuchokera ku Reserve yawo.
Hassan Kajoke Charles Petrol Chimwemwe Idana Nixon Nyasulu
Nyasa Big Bullets yati ipitilira kutenga osewera achisodzera ku timu yake yaying'ono pofuna kupereka danga kwa osewera-wa kuonetsa luso lawo.
Timu ya Tigers yati iuza anthu okonda masewero mdziko muno kampani yomwe ithandize timuyi zokambirana zonse zikatha.
Timu ya Kamuzu Barracks yakonza masewero opimana mphamvu kumathero a sabata ino ngati njira imodzi yochita zokonzekera za 2019 season.
Malingana ndi bungwe la Super League of Malawi (Sulom) mpikisano wa TNM uzayamba pa 13 April.
Masewero otsegulira mpikisano-wu azakhala apakati pa TN Stars ndi Nyasa Big Bullets ku Kasungu.
Malawi friendlies tn stars vs silver strikers
Asewera liti
Mzuni 0 3 be forward wanders
2018 TNM Super League top goalscorer, Chiukepo Msowoya has again missed a call from Flames head coach, Ronny Van Geneugden.
Simbi has started 2019 season preparations on Tuesday.
In a telephone interview with the club's Technical Director Zimomo Mwanza confirmed the development.
Imvani has commenced 2019 preparations ahead of this years Chipiku Premier Division kickoff.
Publicity Secretary of the team, Ackleo Uledie confirmed this in an interview with Owinna.
Gate Charges of Ntopwa Games is K500.
Ntopwa says it has planned two friendly games ahead of 2019 season kickoff.
Officials at the club says the games are to rate how the team is performing.
Mlatho Mponela will tomorrow play its first friendly game in 2019 season against a TNM Super League side.
Mponela will battle it out with Blue Eagles at Mponela Community Ground.
To see full Flames squad visit our Facebook page @ Owinna.
GOALKEEPERS; Nenani Juwaya (BE FORWARD Wanderers), Hastings Banda (Civil Sporting Club), Ernest Kakhobwe (NMC Bullets) DEFENDERS; Stanley Sanudi( BE FORWARD Wanderers), John Lanjesi(NMC Bullets).
Flames coach RVG has recalled a number of players that will go in camp on Sunday ahead of their last 2019 Afcon qualifier against Morocco next Friday at Bingu National Stadium in Lilongwe.
Kampani ya Rab Processors yasainirana mgwirizano ndi bungwe loyendetsa mpira mdziko muno la FAM kuti izithandiza timu ya Flames ndi madzi okumwa.
Bungwe loyendetsa mpira mdziko muno la Football Association of Malawi (FAM) lero ilengeza kampani yomwe izithandiza timu ya dziko lino.
Bonanza ya matimu amu TNM Super League m'chigawo cha kumpoto ati izichitika chaka chili chonse.
Malingana ndi malipoti ati Bonanza-yi ithandizire kupititsa patsogolo masewero m'chigawo-chi.
Akuluakulu omwe amayendetsa Bonanza ya matimu anayi amu TNM Super League m'chigawo cha kumpoto ati apanga ndalama zokwana 1.9 million Kwacha.
Otchinga pa golo wakale wa Dwangwa United, Charles Thom wasaina contract ya zaka zitatu ndi timu ya Silver Strikers.
Katswiri-yu amasewera-nso timu ya Malawi Under 23.
Timu ya Silver Strikers yati ikufunitsitsa itasaina osewera atatu omwe ndi odziwika bwino season ya 2019 isanayambe. Mlembi wa timuyi, Lawrence Yobe, wauza Owinna kuti ali mkati mokambirana ndi matimu-wa.
Ndime yoyamba ya mpikisano wa Chitipa District Council Under 17 yatha dzulo, Lolemba.
Akuluakulu oyendetsa mpikisano-wu akumana sabata ino kufuna kukambirana za tsiku lomwe ndime ya chiwiri.
BE FORWARD Wanderers izayamba 2019 TNM Super League ndi kusewera ndi timu ya Mzuni pa bwalo la Kamuzu mu mzinda wa Blantyre.
Masewero-wa azaseweredwa Loweluka la pa 13 April.
Akuluakulu oyendetsa timu ya Mzuni atsutsa kuti osewera ena sakuchita nawo zokonzekera kaamba kakusamvana komwe kulipo ku timu-yi.
Timu ya Nyasa Big Bullets idzasewera ndi TN Stars pa masewero omwe azakhale otsegulira ligi ya TNM chaka chino. Malingana ndi kafukufuku wa Owinna masewero-wa azaseweredwa pa 13 April pa bwalo la Kasungu.