Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Timu ya Blue Eagles lero isewera ndi Nkhoma Select pa bwalo la William Murray Secondary School pofuna kupeza ndalama zothandizira Tithandizane Orphanage.
Team ya Malawi imatikwezetsa BP. Bola kungomvera zotsatira osati kuiwonera ikusewera.Imatikhumudwitsa kwambiri.
Osafooka. Ziyamba kuyenda.
Fri 22-03-2019 Malawi vs Morocco @ 3:00 PM CAT @ Bingu National Stadium Gate Charges Open Stands: K1,500 VIP Stands: K6,000 Corporate Box: K100,000 Car Pass: K500.
Osewera a timu ya dziko lino ati akonzeka kugonjetsa timu ya Morocco lero pa bwalo la Bingu mu mzinda wa Lilongwe mu mpikisano wa AFCON.
Timu ya Blue Eagles Lamulungu idzasewera ndi Nkhoma Select pa bwalo la William Murray Secondary School pofuna kupeza ndalama zothandizira Tithandizane Orphanage.
Malipoti akusonyeza kuti osewera wa Griffin Young Stars, Peter Banda, akhoza kupita ku timu ya Silver Strikers.
Timu ya chisodzera ya dziko lino ikuyembekezeka kunyamuka mdziko muno kupita ku Zambia komwe akasewere masewero achibwerenza ndi timu ya U23 ya dziko-lo mu mpikisano wa Afcon.
Malawi U23 head coach, Meke Mwase told Journalist today at Kamuzu Stadium that the team still has chances of progressing to another level despite the loss to Zambia.
Nigeria 3 vs Libya 0
Malawi vs Zambia under 23 resresults
FT: Malawi 0-1 Zambia #AFCONu23
Malawi vs Zambia under 23 res
Tafotokozani azanthu ikuenda bwanji game
Malawi U23 head coach, Meke Mwase says they are ready to face Zambia U23 this afternoon at Kamuzu Stadium.
Mwase believes that his side will emerge victors after 90 minutes.
Before the end of this week, Silver Strikers is expected to travel to Mozambique where they will play two international friendlies.
Blue Eagles is set to release its final 2019-20 squad before the end of this month.
Media Officer of the club, Steve Kumalonje disclosed this to Owinna in an interview.
Blue Eagles on Tuesday signed new players to help them in 2019 season.
Media Officer of the team Steve Kumalonje disclosed this to Owinna in an interview.
Newly signed players for Blue Eagles 2/2: 5. Hezekiah Chimseu, Chilimampunga (Mtandire) 6. Foster Bitoni, Mtsiriza Utd 7. Onesimo Mbendera, Nchalo Utd 8. Misheck Mwachipitsa, Steffolds.
Mussa Manyenje has been left out in 2019-20 Nyasa Big Bullets squad.
This means Manyenje is a free agent and that he can join any team.
Malawi U23 vs Zambia U23, what's your prediction?
Malawi iwina 2-0
Mene ma tikiti a masewero-wa akugulitsidwira; Open Stands: K1,000 + Vital Water, MBC Stands: K2,000 + Vital Water, Covered Stands: K3,000 + Vital Water, VIP Stands: K5,000 + Vital Water.
Bungwe loyendetsa mpira mdziko muno lero lichititsa msonkhano wa wolemba nkhani pomwe anene kampani ina yomwe azigwira nayo ntchito. Msonkhano-wu uchitikira ku Chiwembe ndipo uyamba 10 koloko mawa uno.
Timu ya Zambia yafika mdziko muno pomwe mawa ikuyembekezeka kusewera ndi timu ya chisozdera ya dziko lino, Malawi U23.
Masewero-wa azachitikira pa bwalo la Kamuzu mawa mu mzinda wa Blantyre.
Yamikani Chester afika lero mdziko muno kuchokera ku USA komwe akusewera mpira wake.
Chester akuyembekezeka kuchita nawo zokonzekera ndi timu ya Flames yomwe ili mu camp pakadali pano.
Miracle Gabeya komanso Nenani Juwaya alephera kuyamba nawo zokonzekera ndi timu ya Flames Lolemba kaamba koti ndi ovulala.
Timu ya Mafco yati zokonzekera zake zikuyenda bwino pomwe ati akhulupilira kuti akhala ndi season yopambana mu ligi ya Chipiku.
Mmodzi mwa aphunzitsi a Flames, Peter Mponda, wati zokonzekera za timuyi zayamba bwino dzulo, Lolemba.
Malingana ndi Mponda pafupifupi osewera onse ayamba nawo zokonzekera-zi.
Is the time of kick off the match between Malawi vs Zambia Under 23, 4:30pm?
Corrected. The game will kick off at 2:30 pm. Thanks.
Fixtures ya ma games a Malawi under 23 and National Team pkease muyikeko it helps us with other issues.
Tayika ma fixtures pano. Thanks for your request.
FAM says all is set for Malawi Under 23 game this week.FAM says it will start selling tickets of the game today.On Wednesday Malawi U23 will play against Zambia at Kamuzu Stadium.
Silver strikers will release its final Squad before the end of this week.
According to Lawrence Yobe, technical panel is compiling the squad.
Silver Strikers has finalised signing of players from other clubs.
Lawrence Yobe said this in an interview with Owinna.
According to Yobe players that the technical panel wanted have been signed.
Silver Strikers is remaining with two signings before the season starts.
According to Yobe discussions are at advanced stage with the players.
Silver Strikers played against Area 18 Stars on Saturday and won 15 - 0.
And yesterday they won 4 - 0 against Dzaleka Select.
Chitipa District Council Under 17 second round is expected to commence this coming weekend.
Officials have confirmed about the development to Owinna.