Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Timu yomwe yangolowa kumene mu TNM Super League kuchokera m'chigawo cha kumpoto yalephera kupambana masewero ali onse mu Bonanza ya matimu anayi amu ligi ya TNM.
Masewero ena mu Chitipa District Council Under 17 analephereka zomwe zipangitse kuti ndime yoyamba ya mpikisano-wu ithe mawa, Lolemba.
Nthambi yomwe imaona za club licencing ku FAM ikhala ikuunika mmene matimu achitira pofuna kukwaniritsa ndondomeko-yi.
Malingana ndi malipoti, FAM iunika matimu onse 16 amu TNM Super League.
Silver Strikers ikumana ndi timu ya TN Stars pa bwalo la Kasungu lero masana.
Masewero-wa akonza ndi a Hope Ministries pofuna kupeza ndalama zothandizira ntchito zawo.
Timu ya chisodzera ya dziko lino ya Malawi U23 ipitilire kuchita zokonzekera zake patsogolo pa masewero awo ndi Zambia. Timuyi yafika mdziko muno kuchokera ku Egypt komwe inasewera masewero ake omaliza.
Congratulations @lukasi.gk.lubeni for the correct Chitipa vs Moyale prediction. owinna.com
Gate Charges: Open Stand: K1,000
Pa tsiku pazikhala masewero awiri ndipo kuti ndalama yomwe munthu azilipira-yi akaonera masewero onse.
Masana a lero matimu m'chigawo cha kumpoto omwe amasewera mu TNM Super League akhale akulimbirana ukatswiri wa Bonanza yomwe yakonzedwa m'chigawo-chi.
Malawi Under 23 national football team tsopano yamaliza masewero ake opimana mphamvu ndi matimu akunja pa ulendo wake wa sabata zitatu.
First Match Dwangwa United 0 - 3 Silver Strikers (Zikani Kasambala, Victor Limbani [2])
Second Match Dwangwa United 2 - 0 Silver Strikers ?
Timu ya Silver Strikers inapambana masewero ake oyamba ndi Dwangwa United ndi zigoli zitatu kwa dhu. Pa masewero-wa Zikani Kasambala anamwetsa chigoli chimodzi, Victor Limbani anagoletsa zigoli ziwiri.
FT: Egypt U23 2 - 0 Malawi U23
Timu ya chisodzera ya dziko lino yagonja pa masewero ake ndi anzawo a Egypt ndi zigoli ziwiri kwa dhu.
Former Nyasa Big Bullets midfielder, Raquib Lulu Milanzi, has been unveiled as Airtel Top 8 brand ambassador.
Milanzi also played for Civil Sporting, Nairobi City Stars, Tuska and Caps United.
Officials from Silver Strikers say their game against BE FORWARD Wanderers in Airtel Top 8 will be pay back time. The officials say they want to revenge the FISD Challenge Cup Finals defeat.
Airtel Top 8 is scheduled to commence in April after a successful draw yesterday at Mpira Village, Chiwembe in Blantyre.
FAM is today expected to release fixed dates for first leg games.
Hope Ministries in Kasungu on Sunday has organised a Bonanza aiming to raise funds for its activities.
TN Stars will battle it out with Silver Strikers in the Bonanza.
Silver Strikers will play its first friendly game in 2019 tomorrow, Saturday.
The central bankers are scheduled to rock horns with Dwangwa United at Chitowe Stadium.
Airtel Top 8 draw
Silver Strikers vs BE FORWARD Wanderers,
TN Stars vs Karonga United,
Mzuni vs Civil Sporting,
Kamuzu Barracks vs Masters Security.
Umenewo nde osayamba
A solom perekan fixer mwachangu kaa mwatan
Posachedwapa tikupatsani fixture yonse koma masewero otsugulira ligi ndi a Bullets vs TN Stars pa 13 April ku Kasungu
Ntchito yoyendera mabwalo omwe matimu agwiritse mu season ya 2019 itha lero m'chigawo cha kummwera.
Akuluakulu ochokera ku FAM lero amaliza ntchito-yi ndi kuyendera bwalo la Kalulu komanso la Mulanje.
Football Association of Malawi (FAM) yati bwalo la Chilomoni siligwiritsidwanso ntchito season ino maka mu TNM Super League.
Lero matimu omwe asewere mu mpikisano wa Airtel Top 8 adziwa mmene masewero awo oyamba akhalire.
When is superleague starting?
The 2019 TNM Super League season will start on 14 April.
KODI # TNM SUPER LEAGUE IZAYAMBA LITI?
Asintha izayamba pa 13
Former Nyasa Big Bullets defender Emmanuel Zoya has signed a 1 year deal with Civil Sporting.
Zoya returned to his previous club after being released by Bullets.
Blessings Kameza and Damiano Kunje are doing trials at Civil Sporting.
Club officials have confirmed about the development to Owinna.
Football Association of Malawi (FAM) says it will embark on a project of constructing modernised stadiums in all regions of the country.
2019 Airtel Top 8 draw will take place on Thursday from 10 am at Mpira Village in Blantyre.
Football Association of Malawi (FAM) officials have confirmed the development.
Blue Eagles game against the champions of Nyasa Big Bullets Challenge Bonanza, Clube Ferroviario De Nampula has been cancelled.
Media Officer of the team, Steve Kumalonje confirmed the development.
Mphunzitsi wa timu ya Wanderers, Yasin Osman, wati waphunzira zambiri pa mpikisano wa Nyasa Big Bullets Challenge Bonanza.
Mpikisano wa Nyasa Big Bullets Challenge Bonanza uchitika kwa zaka zitatu zomwe zikubwera-zi.
BE FORWARD Wanderers has unveiled a new kit for 2019 season. They have orange jersey to be used at home and black for away games. Goalkeepers will be using green and white jerseys.
Omwe amayendetsa Nyasa Big Bullets Challenge Bonanza ati ndi okhutira ndi mmene mpikisano-wu wayendera.
Katswiri wosewera pakati mu timu ya Nyasa Big Bullets, Henry Kabichi, komanso wosewera wa Ferroviaro de Nampula, Milambo, ndiwo akhala akatswiri omwe amwetsa zigoli zochuluka mu mpikisano-wu.
Ferroviaro de Nampula are the champions of Nyasa Big Bullets Challenge Bonanza after topping the table with 5 points.
Amene awine gemu ya Bullets vs Wanderers atenga chikho. Wanderers itapanga draw yosachepera zigoli zitatu ingathenso kukhala champion.
Chicken Inn from Zimbabwe has failed to win a game in Nyasa Big Bullets Challenge Bonanza.
Chicken Inn has finished the competition with a point after a 1 all draw against Ferroviaro De Nampula.
The team that wins Blantyre Derby has the chance to be crowned champions of Nyasa Big Bullets Challenge Bonanza.
Wanderers can also be crowned champions if they draw with at least 3 goals.
Zkuthekela bwanj
Zikuti bwanji pano
Katswiri wa Nyasa Big Bullets Challenge Bonanza adziwika lero pa bwalo la Kamuzu mu mzinda wa Blantyre pomwe pakhale masewero omaliza a mpikisano-wu.
Malawi Under 23 national football team ili mdziko la Egypt komwe ikuyembekezeka kusewera masewero opimana mphamvu ndi timu ya chisodzera ya dziko-lo.
Malawi U23 yafika ku Egypt Lamulungu usiku.
Tsiku lomwe mpikisano wa TNM Super League umayembekezeka kuyamba lasintha kuchoka pa 6 April kufika pa 14 April.
Mlembi wa Super League of Malawi (Sulom), Williams Banda, watsimikiza za nkhaniyi.
Ndime yoyamba ya mpikisano wa Chitipa District Council Under 17 ifika kumapeto sabata ino, Loweluka.
Akuluakulu omwe akuyendetsa mpikisano-wu atsimikiza za nkhaniyi.
Tiwuzeni za Mali results
Onani pa ma results onse taika za ku Belgium