Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
BE FORWARD Wanderers and Nyasa Big Bullets have pocketed 5 million Kwacha each for their participation during independence celebrations.
Ndipo masewero opimana mphamvu apakati pa timu ya Bullets ndi Mlatho Mponela nawo alephereka.
Akuluakulu a matimu-wa sanapereke zifukwa zomwe zalepheretsa masewero-wa.
Timu ya Silver Strikers yakana kusewera masewero opimana mphamvu ndi timu ya Bullets ponena kuti osewera ake ambiri ndi ovulala.
Matimu awiri-wa amayembekezeka kusewera masewero-wa mawa.
0885258969