Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Timu ya Tigers yati ikhale ikuuza aMalawi tsogolo la timuyi mu 2019 season, maka kampani yomwe ithandize timuyi. Izi zikutsatira kusiya kwa kampani ya Azam kuthandiza timuyi.
Civil Sporting tomorrow will play a friendly match against Dedza Dynamos.
Civil Sporting officials have confirmed about the development to Owinna.
Nduna yoyang'anira za masewero, Grace Obama Chiumia, yapempha anthu a luso mdziko muno kugwiritsa bwino luso lawo pofuna kuthandizira kutukula chuma cha dziko lino.
Silver Strikers started their 2019 preparations on Tuesday.
The club has received players from Nigeria and Cameroon who are on trials.
Blue Eagles is hunting signatures of new players, in particular, strikers.
Media Officer of the club, Steve Kumalonje, confirmed the development saying 2019 preparations are progressing well.
Timu ya Mchinji Boma Stars, yomwe imasewera mu Chipiku Premier Division, ikuvutikabe kuti ipeze oyithandiza pomwe ligiyi ikhale ikuyamba posachedwapa. Mlembi wa timuyi, Lyson Tasauka, watsimikiza izi.
Timu ya Malawi Under 23 lero ipitilira kuchita zokonzekera zake mdziko la Belgium.
Dzulo timuyi inaonera masewero amu mpikisano wa Europa a KRC GENK ndi Slavia Praag.
Malipoti akusonyeza kuti mavuto azachuma ku timu ya Dwangwa adakalipo pomwe patsala mwezi umodzi kuti TNM Super League iyambe. Timu ya Dwangwa siinapezebe ndalama zoyendetsera timuyi.
Bungwe loyendetsa mpira kuno ku Malawi, la Football Association of Malawi (FAM), lati ndilodzipereka kugwira ntchito limodzi ndi kampani zina pofuna kutukula mpira mdziko muno.
Yemwe anali wotsogelera osewera anzake (Captain) mu timu ya Nchalo United, Felix Katongo Kamwendo, sanapeze timu yoti atumikire mu season ya 2019.
Please note that players who performed well in SIMSO Premier League are yet to receive their awards.
NRFA officials have confirmed this saying they will set another day for individual awards.
FAM says this years Charity Shield will focus on mobilizing football fans and the general public to take decisive actions on the killings and abductions of people with albinism.
Teams to participate this year's FAM Charity Shield are; Blue Eagles, BE FORWARD Wanderers, Nyasa Big Bullets, Masters Security.
BE FORWARD Wanderers will play a friendly game against newly promoted team from the Southern Region Premier League, Ntopwa.
Malawi Under 23 team will today watch a Europa League Game between KRC Genk vs Slavia Praag in Belgium.
Timu ya Malawi Under 23 lero masana isewera masewero ake achiwiri mdziko la Belgium ndi PSV.
Timu-yi inagonja masewero ake oyamba dzulo ndi zigoli zitatu kwa chimodzi pomwe amasewera ndi STVV.
Bonanza yomwe timu ya Nyasa Big Bullets ichititse, padzakhala matimu anayi, awiri ochokera kunja kwa dziko lino, ndipo kuno ku Malawi izakhala Noma ndi Bullets.
Mkulu woyendetsa ntchito za Nyasa Big Bullets, Fleetwood Haiya, wati zokonzekera zonse za bonanza yomwe akonza kumayambiliro a mwezi wa March zili mchimake.
New Executive Committee at Silver Strikers: Chair: Peter Chando, Vice: Alick Tahuna, GS: Laurence Yobe, Vice: Innocent Kadammanja, Treasurer: Judith Kachimanga, Vice: Patrick Mbiliyakula.
Executive Committee yatsopano ya Silver Strikers lero ikumana ndi Board of Trustees ya timu-yi kukambirana m'mene ayendetsere timu ya Silver Strikers chaka chino.
Timu ya Silver Strikers yayamba zokonzekera zake za 2019 season dzulo mu mzinda wa Lilongwe.
Kwa nthawi ku timu-yi kunali kukokana-kokana pa anthu omwe ayendetse timu-yi chaka chino.
Timu ya dziko lino ya osewera achisozera ya Malawi U23 yagonja masewero ake oyamba ku Belgium ndi zigoli zitatu kwa chimodzi.
Malawi U23 imasewera ndi STVV
Silver Strikers will start 2019 season preparations today, Tuesday.
Club officials have confirmed about the development.
Timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino ya Malawi Under 23 lero masana isewera masewero ake oyamba mdziko la Belgium ndi STVV. Timu ya dziko lino-yi inachita zokonzekera zake kukonzekera za masewero-wa.
Ligi ya m'chigawo cha kumpoto ya SIMSO ipitilira kulandira ndalama zochepa kuyelekeza ndi ma ligi ena mdziko muno.
Izi zikutsatira kusakambapo kali konse kuchokera ku sponsor wa ligi-yi.
Otsatira timu ya Wanderers ati akufunitsitsa timu-yi itatenga chikho cha TNM Super League komanso kuteteza FISD Cup chaka chino.
Mlembi wa masapota wa timu-yi, Sam Mponda, ndiye wanena izi.
Akuluakulu ena oyendetsa matimu m'chigawo cha kumwera ati ganizo loti timu yomwe yatuluka mu Super League isamabwelere ku ligi ya ThumbsUp Premier Division silabwino.
Otsatira timu ya Wanderers ati ndi okhutira ndi m'mene timu yawo yachitira pa msika pogula osewera ku matimu ena.
Mlembi wa masapota wa BE FORWARD Wanderers, Sam Mponda, ndiye wanena izi.
ndikhani yosakhaldwino
Osewera yemwe amasewera kutsogolo mu timu ya BE FORWARD Wanderers chaka chatha, Peter Wadabwa, ali ku Mozambique komwe akuyang'ana timu yoti asewere.
Nyasa Big Bullets Reserve is inviting interested players who want to join the club for trials today at Kamuzu Stadium. Club officials have confirmed this saying the training session will start at 2 PM.
Matimu amu TNM Super League awaphunzitsa njira zoyenera kutsata pofuna kukwaniritsa ndondomeko ya Club Licensing.
Timu ya Dwangwa United, pomwe ikufuna kuyamba zokonzekera zake mawa, yati ili chikhulupiliro kuti anthu okhala m'madera ozungulira komwe timuyi imachokera aithandiza ku mbali ya zachuma.
Malawi Under 23 National Football Team has safely arrived in Belgium.
Officials have confirmed this to Owinna saying the Junior Flames will be in Belgium for 2 weeks.
Silver Strikers will start 2019 season preparations tomorrow, Tuesday.