Timu ya Silver Strikers yalengeza kuti katswiri wawo wotseka kumbuyo Nickson Mwase waonjezera mgwirizano wa zaka ziwiri ndi timuyi.
Katswiriyu anali ndi mgwirizano womwe umatha mu mwezi wa April ndipo anakhudzidwa kwambiri ndi nkhani yoti akuchoka kupita ku FCB Nyasa Big Bullets.
Zateremu, iye akhalabe kutimuyi mpaka mu chaka cha 2027.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores