Timu ya Dedza Dynamos yasaina katswiri wa kale wa Mighty Wanderers, Misheck Botoman, yemwe atumikire timuyi mu Chigawo chachiwiri cha ligi ya chaka chino.
Botoman wasaina mgwirizano wa miyezi isanu ndi umodzi kutimuyi ngati wa ulere kutsatira kuti anachoka ku timu ya Creck Sporting Club atathetsa mgwirizano wake ndi timuyo.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores