Timu ya Dedza Dynamos yalowa mu mgwirizano ndi Goshen City yomwe tsopano izikhuthura ndalama zokwana K2 billion kwa zaka ziwiri kutimuyi.
Mkulu wa Goshen City, Prophet Shepherd Bushiri lachiwiri anakasaina mapepala ndi timuyi kutsimikiza mgwirizanowu.
Zateremu, timuyi iyamba kutchedwa kuti Goshen City Dedza Dynamos kamba ka mgwirizanowu.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores