Timu ya Mighty Tigers yatenga katswiri womwetsa zigoli Mwai Banda ngati mbali yokonza vuto lakumwetsa zigoli kutimuyi.
Iye wapita kumpanda pomwe wasiyana ndi timu ya Ekhaya kamba kosowa nthawi yosewera kutimuyi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores