Timu ya Chitipa United yalemba uthenga wopepesa kamba ka mchitidwe umene mphunzitsi wawo, Kondwa Ikwanga, anachita pamene anagonja 2-0 ndi timu ya FCB Nyasa Big Bullets.
Timuyi yati yakambitsana ndi mphunzitsiyu pofuna kuonetsetsa kuti mchitidwewu usadzachitikenso.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores