NKHANI
Creck Sporting Club yalengeza kuti yasaina a katswiri awiri, Kondwani Chilembwe komanso Tathedwa Willard.
Osewera awiriwa apita kutimuyi mwaulere ndipo asaina mgwirizano wa zaka ziwiri aliyense.
Chilembwe anali ku Bangwe All Stars chaka chatha yomwe inatuluka mu ligi ndipo Willard anali pa ngongole ku timu yomweyi chaka chatha Kuchokera ku Silver Strikers yomwe mgwirizano wake watha.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores