Timu ya Nyasa Big Bullets ilinawo pa mndandanda wa matimu amene atenge nawo gawo mu mpikisano wa CECAFA Kagame Cup m'dziko la Tanzania kuyambira pa 6 July mpaka pa 22 July 2024.
Ena mwa ma timu omwe ayitanidwa nawo ku mpikisanowu ndi a TP Mazembe kuchoka ku DRC komanso Red Arrows ya ku Zambia.
Timu ya Bullets siidayankhulepo kanthu pankhaniyi koma chikalata chomwe atulusa a CECAFA chikuonesa kuti timuyi yavomera kutero
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores