Timu ya Blue Eagles yati woimbira masewero a mpira wamiyendo Chikumbutso Simbi asazaimbireso masewero a timuyi.
Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe timuyi yatulutsa chomwe wasainaira ndi wapampando wa timu ya Blue Eagles Alexander Ngwala.
A Ngwala ati woimbirayu anaphwanya dala malamulo ena pamene amaimbira masewero apakati pa timuyi ndi Nyasa Big Bullets.
Bullets inachita kuchokera kumbuyo kubwenza chigoli pamene Blue Eagles imatsogola kuti masewero-wa athere 1-1.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores