Bungwe la Football Association of Malawi (FAM) lero lichititsa msonkhano wa wolemba nkhani ku Amaryllis Hotel mu mzinda wa Blantyre.
Msonkhano-wu achititsa pamodzi ndi bungwe la Super League of Malawi (Sulom).
Cholinga cha msonkhanowu sichikudziwika padakali pano koma pali kuthekera koti mabungwe awiriwa akufuna kulengeza za mgwirizano watsopano wa ligi ya TNM.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores