Timu ya Civil Service United yatsutsa malipoti oti akufuna kulemba ntchito wachiwiri kwa mphunzitsi wa Karonga United Oscar Kaunda.
Mlembi wa timu ya Civo, Ronald Chiwaula wati padakali pano apitilira ndi aphunzitsi awo omwe ndi Franco Ndawa komanso Elia Kananji.
Malipotiwa anafala masamba a mchezo pomwe a Kaunda anavala mayala amakaka a timu ya Civo pamene timuyi imasewera ndi Mzuzu Warriors.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores