Bungwe lothana ndi katangale komanso ziphuphu la ACB lati likuptilira ndi kafukufuku wake pa nkhani yokhudza matimu ena kupereka ndalama kwa oimbira kuti azichita bwino m'masewero awo.
Football Association of Malawi (FAM) inalembera ACB kuti ifufuze malipotiwa pambuyo poti woimbira masewero a mpira wa miyendo mdziko muno, Arthur Chilimba amafuna kutchula anthu omwe akuchita izi.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores