Kapinga wakula pa bwalo la Bingu pamene adindo oyang'anira bwaloli sakuchitapo kanthu.
Mwezi wa December, akuluakulu oyang'anira bwaloli anauza aMalawi kuti akhale akukonza zinthu zina pa bwaloli.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores