Matimu a Bullets ndi Wanderers akumana masana-wa mu mpikisano wa Energem International Bonanza.
Awa ndi masewero omaliza pakati pa matimu awiri-wa.
Masewero-wa achitikira pa bwalo la Kamuzu.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores