Walter Nyamilandu lero ndi tsiku lomaliza kugwira ntchito ku kampani ya Illovo pomwe wati akufuna kulunjika chidwi chake potukula masewero a mpira.
Izi zatsimikizidwa m'chikalata chomwe kampaniyi yatulutsa chomwe chatsimikiza za kusiya ntchito kwa a Nyamilandu.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores