Banki ya FDH yakhazikitsa chikho cha 90 million Kwacha chomwe chizitchedwa FDH Bank Cup.
Akuluakulu a banki-yi akhazikitsa chikho-chi mu mzinda wa Blantyre.
Matimu 16 a zigawo akuyembekezeka kumatenga nawo mbali mu chikho-chi.
Opambana chikho-chi akuyembekezeka kumalandira 25 million Kwacha.
Banki ya FDH ikhala ikuthandiza chikho-chi kwa zaka 5.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores