Login with Facebook to post predictions, updates & live scores
Wats up link
Singh
League yavuta guys
am enjoying this webpage
Tnm super league live scores
Noms
WANDAR WOYE
Kuli mpungwepungwe ku VIP pomwe otsatira Walter Nyamilandu amalimbana ndi anthu ena omwe amamunyoza.
Pakadali pano Nyamilandu ndi akuluakulu ena achokapo ku Kamuzu Stadium.
WATER WAKONDA KOMA JEMUS NDIYE
Silver Strikers has signed Maxwell Phodo.
Phodo was playing for Mzuni.
Silva. 2-0 .kalonga . ine fernando wa ma bankas chipindu mozambiQI SILVA. WOYE.E.E! prediction
Some things you might wish to know for the COSAFA Youth Championship; Last year, Malawi did not progress to the next round of the competition. Angola won the competition after qualifying as runners up
Flames coach, DeKlerk Msakakuona, is today expected to release a 20 man squad which will participate in the COSAFA Youth Championship.
Msakakuona said this is in line with the competition rules.
Vincent Nyanguluβs return boosts Wanderers - The Times Group Malawi TNM Super league leaders Be Forward Wanderers have received a timely boost ahead of the Blantyre derby following the return of... times.mw
bb ikuwina timwa wakaka
asika alikutipano
Vote player of the month of September:
China Chirwa Ndaona Daisi Peter Banda Chifuniro Mpinganjira Muhammad Sulumba.
peter banda
Contenders of FAM President position come December as of now: Walter Nyamilandu (Current FAM President), James Mwenda (Current FAM President), Moses Mkandawire, Alufeyo Chipanga.
Katswiri pa nkhani za masewero, Higer Mkandawire, wati ndi zovuta kuti mpira ungasinthe ngati Walter Nyamilandu atasankhidwanso ngati otsogolera bungwe la FAM.
Stay tuned in to Owinna.com as Walter Nyamilandu will speak to the public using some local media houses on his stand in the forthcoming elections of FAM.
Mphunzitsi wa Silver Strikers, Abbas Makawa, wati achirimika kuti zinthu ziyambireso kuyenda ku timuyi.
Makawa amayankhula izi kutsatira kugonja ndi Civo.
A Makawa ati ndi khumbo lawo kutenga ligi.
Nyasa Big Bullets and Flames captain, John Lanjesi, will miss the rest of the season.
This has been confirmed by Bullets officials.
The player is expected to undergo operation for his knee injury.
Mphunzitsi wa Flames U17, Declerk Msakakuona, akuyembekezeka kutulutsa mndandanda wa osewera omwe atenge nawo mbali mu mpikisano wa COSAFA Youth Championship.
Mphunzitsi wa timu ya mpira was chisodzera ya Flames, Declerk Msakakuona, wati ndi wosangala ndi momwe zokonzekera za timuyi zikuyendera pomwe wati osewera akuikapo mtima.
Div1