Kusowa kwa ndalama ku ligi ya SIMSO ati kwapangitsa oyendetsa ligi-yi kulephera kukwanilitsa zinthu zina zofunikira.
Ollens Msonda, wanena izi patsogolo potsegulira ndime yachiwiri, Loweluka.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores