Bungwe la Football Association of Malawi lati bwalo la Kamuzu mu mzinda wa Blantyre siloyeneranso kuchititsa masewero akulu akulu kuphatikizapo masewero a Big Bullets ndi Mighty Wanderers.
FAM lati bwalo la Kamuzu silibwino kuti lingachititse masewero akuluwa.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores