Kampani ya Castel kuyambira chaka chino ibweletsa chikho chatsopano chomwe chizitchedwa Castel Challenge Cup.
Matimu oposa 2000 ndi omwe atamakanganilane chikhochi kuchokera ku district mpaka national level. Ndalama zokwana 1 billion ndi zomwe zingagwilisidwe ntchito kwa zaka zitatu,MK320 million pachaka.
Katswiri wa chikhochi azilandira ndalama zokwana MK50 million.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores