Petro wasewera masewero ake oyamba
Otchinga kumbuyo wadziko lino yemwe akusewera kunja ku Romania mu timu ya FC Botosani dzulo anasewera masewero ake oyamba chibwelereni kutimuyi.
Petro yemwe akuvala jezi #28 anasewera masewero onse pamene Botosani inalephelana ndi Mioveni 1-1. Botosani yamaliza pa number 11 ndi 32 points pamene ikudikira kuti iyambe ndime ina yozigulira malo.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores