Ulendo uli lero
Mkulu ofalitsa nkhani ku bungwe la Football Association of Malawi (FAM) watsimikiza kuti lero pa 11 March team ya Flames ikhala ikupita ku Saudi Arabia.
Izi zikuza timuyi italephera kunyamuka dzulo ndi zana kamba kazitupa zoyendela. Malawi ikupita ku Saudi Arabia ngati mbali imodzi yokonzekela masewero awo omwe ali nawo kumapeto a mwezi uno ndi Egypt
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores