Osewera 11 akale a Mighty Mukuru Wanderers ayitengela timuyi ku khothi chifukwa chakusalipilidwa komanso mu contract yawo munali zinthu zina zomwe Wanderers sinakwanalise.
Osewerawa ndi Lucky Malata, Ted Sumani, Lloyd Mugala, Mike Kaziputa, Simeon Singa, Pilirani Mapira, Aubrey Maloya, Hankey Machila, Riaz Juama, Francis Mlimbika ndi Bongani Kaipa.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores