Katswiri wa FCB Nyasa Big Bullets, Hassan Kajoke, waonjezera mgwirizano wake ndi zaka ziwiri kutimuyi.
Iye akhalabe kutimuyi mpaka mu chaka cha 2028.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores