Timu ya Civil Service United yatsimikiza kuti mtsogoleri watimuyi, Righteous Banda, waonjezera mgwirizano wake ndi zaka ziwiri.
Banda, yemwe anatsiliza mwapamwamba mu ligi ya chaka chatha, akhalabe kutimuyi mpaka mu chska 2028.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores