NKHANI
Timu ya Bangwe All Stars yalengeza kuti ikuyamba zokonzekera zake lachitatu pa 04 March 2026.
Iwo akuyitana osewera omwe akufuna kutumikira timuyi kufika pa bwalo la Kamuzu kudzayesa mwayi koma adzatenge ndalama yawo yoyendera pakuti sadzabwenzeredwa.
Timuyu yati mwayiwu ndi wa osewera okha omwe ali mu mzinda wa Blantyre.
Bangwe All Stars imasewera mu ligi yachiwiri yaikulu ya dziko lino ya NBS Bank National Division.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores