Timu ya Mighty Wanderers yalengeza kuti wachiwiri kwa mphunzitsi wawo, MacDonald Nginde Mtetemera, wasaina mgwirizano woonjezera wa zaka ziwiri ndi timuyi.
Iye wathandizira timuyu kutenga ligi yomwe imathandizidwa ndi kampani ya TNM.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores