Timu ya Mighty Wanderers yalengeza kuti mphunzitsi wawo wamkulu, Bob Mpinganjira, waonjezera mgwirizano wake ndi zaka ziwiri.
Iye anathandizira timuyi kupambana ligi yaikulu ya TNM.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores