Bungwe la Super League of Malawi lavomera pempho la timu ya Mighty Wanderers kuti isasewere lachinayi ndi timu ya Ekhaya FC pokonzekera masewero awo amu FDH Bank ndi timu ya Creck Sporting Club lamulungu.
Timuyinso ili ndi osewera awo atatu omwe anali ndi timu ya Flames ndipo akukonzekera kufika m'dziko muno lero kuchokera ku Tunisia komwe anakagonjako 1-0 ndi timu ya Sao Tome.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores