Timu ya Silver Strikers yatenga mphunzitsi wawo wa kale, Etson Kadenge Mwafulirwa kuti atsogolere timuyi mu mpikisano wa CAF Champions League.
Izi zili chomwechi Kamba koti Peter Mgangira alibe mapepala a chitupa cha CAF A omwe ndi ovomerezeka kwa mphunzitsi mu mpikisanowu.
Login with Facebook to post predictions, updates & live scores